Yesaya 66:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova. Zekariya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+ Maliko 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mwana wa munthu ndiye Mbuye wa sabata.”+
23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova.
16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+