Luka 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+ Machitidwe 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+ Machitidwe 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa m’dzina lake.”+
47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+
12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+
43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa m’dzina lake.”+