Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 20
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 20:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 23-24

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 287

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    3/1/1991, tsa. 31

Chivumbulutso 20:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:3
  • +Ge 3:1
  • +Yoh 8:44
  • +Zek 3:1; Chv 12:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 23-24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 287-288

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    9/1/1989, tsa. 12

Chivumbulutso 20:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:11
  • +Chv 20:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 287-288

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    9/1/1989, tsa. 12

    Kukambitsirana, ptsa. 356-357

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 182-183

Chivumbulutso 20:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 22:30
  • +Mt 19:28; Lu 22:30; 1Ak 6:2
  • +Chv 13:12
  • +Chv 13:15
  • +Chv 13:16
  • +2Ti 2:12; Chv 1:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 288-290

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1990, tsa. 31

    9/1/1989, ptsa. 11-12

Chivumbulutso 20:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 5:28; Mac 24:15; Aef 2:1
  • +Mt 25:46; Chv 20:13
  • +1Ak 15:23, 52; Afi 3:11; 1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 19

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 290

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1998, ptsa. 22-23

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 182

    Kukambitsirana, tsa. 112

Chivumbulutso 20:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:13; 22:7
  • +Chv 13:10
  • +Mt 10:28; Chv 2:11; 20:14
  • +1Ak 15:54
  • +1Pe 2:9; Chv 1:6
  • +Chv 5:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 290-291

    Nsanja ya Olonda,

    9/1/1989, ptsa. 11-12

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 172-173

Chivumbulutso 20:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 19

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291-292

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 183

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/1987, ptsa. 31-32

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

Chivumbulutso 20:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 38:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 19

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2017, tsa. 29

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2015, tsa. 30

    5/15/2006, ptsa. 6-7

    12/1/2002, tsa. 29

    10/15/2000, tsa. 19

    10/15/1988, tsa. 20

    1/1/1987, ptsa. 31-32

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291-292

    Lambirani Mulungu, ptsa. 189-191

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 183

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

    Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 183

Chivumbulutso 20:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 48:35; Chv 21:3
  • +Ahe 12:22; Chv 21:2
  • +2Mf 1:10; Eze 38:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291, 292-293, 304

    Lambirani Mulungu, ptsa. 189-191

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2000, tsa. 19

    2/1/1998, tsa. 22

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

Chivumbulutso 20:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:9
  • +Chv 13:1
  • +Chv 19:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2008, tsa. 7

    4/1/2008, ptsa. 22-23

    5/15/2006, ptsa. 6-7

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    11/1/1997, ptsa. 6-7

    4/15/1993, ptsa. 7-8

    12/15/1988, ptsa. 4-5

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 293-295

    Lambirani Mulungu, ptsa. 189-191

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 88

    Kukambitsirana, ptsa. 147-148

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

    Galamukani!,

    10/8/1986, tsa. 20

Chivumbulutso 20:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 12:23; Chv 4:2
  • +2Pe 3:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 213

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 296

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1991, tsa. 5

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 181

Chivumbulutso 20:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:15; Chv 11:18
  • +Eks 32:33; Sl 69:28; Da 12:1
  • +Yoh 5:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 18-19, 26

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2016, ptsa. 29-30

    3/2016, tsa. 22

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, ptsa. 213-214

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2010, tsa. 11

    3/15/2009, tsa. 12

    2/15/2009, tsa. 5

    1/15/2008, tsa. 28

    5/1/2005, tsa. 19

    8/15/1998, tsa. 30

    7/1/1998, tsa. 22

    8/1/1991, tsa. 6

    9/1/1987, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 296-297, 298-300, 310

    Lambirani Mulungu, tsa. 87

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 181-183

    Kukambitsirana, tsa. 111

Chivumbulutso 20:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:42
  • +Yoh 5:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2008, tsa. 9

    5/1/2005, tsa. 19

    6/1/2000, tsa. 6

    4/1/1999, ptsa. 18-19

    8/1/1991, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 297

    Lambirani Mulungu, tsa. 87

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 181-182

    Kukambitsirana, ptsa. 111, 113

Chivumbulutso 20:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 25:8; Aro 5:12; 1Ak 15:26
  • +Chv 2:11; 20:6; 21:8
  • +Mt 5:22; 18:9; Yak 3:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2006, tsa. 31

    4/1/1999, ptsa. 18-19

    8/1/1991, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 300

    Lambirani Mulungu, ptsa. 86-87

    Kukambitsirana, tsa. 113

    Galamukani!,

    10/8/1986, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 20:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:8
  • +Miy 10:7; Chv 21:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 5

    8/1/1991, tsa. 6

    9/1/1987, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 300

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 183

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 20:1Chv 9:1
Chiv. 20:2Chv 12:3
Chiv. 20:2Ge 3:1
Chiv. 20:2Yoh 8:44
Chiv. 20:2Zek 3:1; Chv 12:9
Chiv. 20:3Chv 9:11
Chiv. 20:3Chv 20:7
Chiv. 20:4Lu 22:30
Chiv. 20:4Mt 19:28; Lu 22:30; 1Ak 6:2
Chiv. 20:4Chv 13:12
Chiv. 20:4Chv 13:15
Chiv. 20:4Chv 13:16
Chiv. 20:42Ti 2:12; Chv 1:6
Chiv. 20:5Yoh 5:28; Mac 24:15; Aef 2:1
Chiv. 20:5Mt 25:46; Chv 20:13
Chiv. 20:51Ak 15:23, 52; Afi 3:11; 1At 4:16
Chiv. 20:6Chv 14:13; 22:7
Chiv. 20:6Chv 13:10
Chiv. 20:6Mt 10:28; Chv 2:11; 20:14
Chiv. 20:61Ak 15:54
Chiv. 20:61Pe 2:9; Chv 1:6
Chiv. 20:6Chv 5:10
Chiv. 20:8Eze 38:15
Chiv. 20:9Eze 48:35; Chv 21:3
Chiv. 20:9Ahe 12:22; Chv 21:2
Chiv. 20:92Mf 1:10; Eze 38:22
Chiv. 20:10Chv 12:9
Chiv. 20:10Chv 13:1
Chiv. 20:10Chv 19:20
Chiv. 20:11Ahe 12:23; Chv 4:2
Chiv. 20:112Pe 3:7
Chiv. 20:12Yoh 5:29
Chiv. 20:12Mac 24:15; Chv 11:18
Chiv. 20:12Eks 32:33; Sl 69:28; Da 12:1
Chiv. 20:13Mac 10:42
Chiv. 20:13Yoh 5:29
Chiv. 20:14Yes 25:8; Aro 5:12; 1Ak 15:26
Chiv. 20:14Chv 2:11; 20:6; 21:8
Chiv. 20:14Mt 5:22; 18:9; Yak 3:6
Chiv. 20:15Chv 17:8
Chiv. 20:15Miy 10:7; Chv 21:8
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 20:1-15

Chivumbulutso

20 Ndipo ndinaona mngelo akutsika kuchokera kumwamba ali ndi kiyi wa paphompho+ ndi unyolo waukulu m’dzanja lake. 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000. 3 Ndipo anamuponyera m’phompho+ ndi kutseka pakhomo pa phompholo n’kuikapo chidindo kuti asasocheretsenso mitundu ya anthu kufikira zitatha zaka 1,000. Pambuyo pake, adzamasulidwa kanthawi kochepa.+

4 Kenako ndinaona mipando yachifumu+ ndi amene anakhalapo. Iwo anapatsidwa mphamvu yoweruza.+ Ndiyeno ndinaona miyoyo ya amene anaphedwa ndi nkhwangwa chifukwa cha kuchitira umboni za Yesu, ndi kulankhula za Mulungu. Ndinaonanso anthu amene sanalambire chilombo+ kapena chifaniziro chake,+ ndipo sanalandire chizindikiro pamphumi pawo ndi padzanja pawo.+ Iwo anakhalanso ndi moyo ndipo analamulira monga mafumu+ limodzi ndi Khristu zaka 1,000. 5 (Akufa+ enawo sanakhalenso ndi moyo kufikira zitatha zaka 1,000.)+ Uku ndi kuuka koyamba+ kwa akufa. 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+

7 Tsopano zikadzangotha zaka 1,000, Satana adzamasulidwa m’ndende yake, 8 ndipo adzatuluka kukasocheretsa mitundu ya anthu kumakona onse anayi a dziko lapansi. Mitunduyo ndiyo Gogi ndi Magogi, ndipo adzaisonkhanitsa pamodzi kunkhondo. Kuchuluka kwawo kudzakhala ngati mchenga wa kunyanja.+ 9 Iwo adzayenda n’kufalikira mpaka kumbali zonse za dziko lapansi, kenako adzazungulira msasa wa oyera,+ ndi mzinda wokondedwa.+ Koma moto udzatsika kuchokera kumwamba ndi kuwapsereza.+ 10 Mdyerekezi,+ amene anali kuwasocheretsa, adzaponyedwa m’nyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wonyenga uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa usana ndi usiku kwamuyaya.

11 Kenako ndinaona mpando wachifumu waukulu woyera, ndi amene anakhalapo.+ Dziko lapansi ndi kumwamba zinathawa+ pamaso pake, ndipo malo a zimenezi sanapezekenso. 12 Ndiye ndinaona akufa, olemekezeka ndi onyozeka,+ ataimirira pamaso pa mpando wachifumuwo, ndipo mipukutu inafunyululidwa. Koma mpukutu wina unafunyululidwa, ndiwo mpukutu wa moyo.+ Ndipo akufa anaweruzidwa malinga ndi zolembedwa m’mipukutuyo, mogwirizana ndi ntchito zawo.+ 13 Nyanja inapereka akufa amene anali mmenemo. Nayonso imfa ndi Manda zinapereka akufa+ amene anali mmenemo. Aliyense wa iwo anaweruzidwa malinga ndi ntchito zake.+ 14 Ndipo imfa+ ndi Manda zinaponyedwa m’nyanja yamoto.+ Nyanja yamoto imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+ 15 Komanso, aliyense amene sanapezeke atalembedwa m’buku la moyo+ anaponyedwa m’nyanja yamoto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena