Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 16
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la 1 Akorinto

      • Kutolera zopereka zopita kwa Akhristu a ku Yerusalemu (1-4)

      • Maulendo amene Paulo ankafuna kuyenda (5-9)

      • Ulendo wa Timoteyo ndiponso wa Apolo (10-12)

      • Malangizo ndiponso kupereka moni (13-24)

1 Akorinto 16:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:17; Aro 15:26; 2Ak 8:3, 4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/1998, tsa. 24

1 Akorinto 16:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,

    11/2023, tsa. 3

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 55

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2013, tsa. 14

    7/15/2008, tsa. 27

    12/1/2002, tsa. 5

    11/1/2002, ptsa. 26-30

    11/1/1998, tsa. 24

    12/1/1994, tsa. 17

    1/15/1992, tsa. 17

    4/15/1991, tsa. 27

    12/1/1989, tsa. 24

    Utumiki wa Ufumu,

    1/2002, tsa. 2

1 Akorinto 16:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 8:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/1998, tsa. 7

    12/1/1989, tsa. 24

1 Akorinto 16:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/1998, tsa. 7

    12/1/1989, tsa. 24

1 Akorinto 16:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:21; 2Ak 1:15, 16

1 Akorinto 16:7

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 20:2

1 Akorinto 16:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:1

1 Akorinto 16:9

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “mwayi.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:10, 11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2008, ptsa. 18-19

    12/15/1990, tsa. 23

1 Akorinto 16:10

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:1, 2
  • +Afi 2:19, 20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2009, ptsa. 14-15

1 Akorinto 16:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:24, 25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, tsa. 22

1 Akorinto 16:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “pitirizani kuchita chamuna.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 5:6
  • +1Ak 15:58; Afi 1:27
  • +Mac 4:29
  • +Aef 6:10; Akl 1:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2015, ptsa. 13-17

    1/1/2003, ptsa. 18-19

    4/1/2002, ptsa. 15, 27-28

    4/15/1990, ptsa. 26-28

    Galamukani!,

    5/8/2000, tsa. 30

    Utumiki wa Ufumu,

    2/2000, tsa. 8

1 Akorinto 16:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 13:4; 1Pe 4:8

1 Akorinto 16:15

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “zipatso zoyambirira.”

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1988, ptsa. 19-20

1 Akorinto 16:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 2:29, 30; 1At 5:12; 1Ti 5:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1988, ptsa. 19-20

1 Akorinto 16:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1988, ptsa. 19-20

1 Akorinto 16:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1988, ptsa. 19-20

1 Akorinto 16:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 16:3, 5; Fili 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2007, tsa. 10

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Akor. 16:1Mac 24:17; Aro 15:26; 2Ak 8:3, 4
1 Akor. 16:32Ak 8:19
1 Akor. 16:5Mac 19:21; 2Ak 1:15, 16
1 Akor. 16:7Mac 20:2
1 Akor. 16:8Mac 19:1
1 Akor. 16:9Mac 19:10, 11
1 Akor. 16:10Mac 16:1, 2
1 Akor. 16:10Afi 2:19, 20
1 Akor. 16:12Mac 18:24, 25
1 Akor. 16:131At 5:6
1 Akor. 16:131Ak 15:58; Afi 1:27
1 Akor. 16:13Mac 4:29
1 Akor. 16:13Aef 6:10; Akl 1:11
1 Akor. 16:141Ak 13:4; 1Pe 4:8
1 Akor. 16:16Afi 2:29, 30; 1At 5:12; 1Ti 5:17
1 Akor. 16:171Ak 1:16
1 Akor. 16:19Aro 16:3, 5; Fili 2
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 16:1-24

Kalata Yoyamba Yopita kwa Akorinto

16 Pa nkhani ya zopereka zopita kwa oyerawo,+ mukhoza kutsatira malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya. 2 Tsiku loyamba la mlungu uliwonse, aliyense aziika kenakake pambali kunyumba kwake mogwirizana ndi zimene angakwanitse, kuti zopereka zisadzaperekedwe nditafika. 3 Koma ndikadzafika kumeneko, ndidzatuma amuna amene mungawavomereze mʼmakalata,+ kuti adzapititse mphatso yanu yachifundoyo ku Yerusalemu. 4 Komabe ngati pangafunike kuti inenso ndidzapite nawo, tidzapitira limodzi.

5 Ndidzabwera kumeneko pochokera ku Makedoniya, chifukwa ndidzadutsira ku Makedoniya.+ 6 Ndidzakhala nanu kumeneko, mwinanso nthawi yonse yozizira, kuti mudzandiperekeze kumene ndizidzapitako. 7 Sindikufuna kukuonani panopa mongodutsa chabe, koma ndikufuna kuti ndidzakhale nanu kanthawi ndithu,+ Yehova* akalola. 8 Koma ndikhalabe kuno ku Efeso+ mpaka pa Chikondwerero cha Pentekosite, 9 chifukwa khomo* lalikulu la utumiki landitsegukira,+ koma pali otsutsa ambiri.

10 Timoteyo+ akadzafika mudzaonetsetse kuti asadzakhale ndi mantha pakati panu, chifukwa iye akugwira ntchito ya Yehova,*+ ngati mmene inenso ndikuchitira. 11 Choncho pasadzapezeke munthu womuderera. Mudzamuperekeze mwamtendere kuti adzabwere kunoko, chifukwa ineyo ndikumuyembekezera pamodzi ndi abale.

12 Ponena za mʼbale wathu Apolo,+ ndinamuchonderera kwambiri kuti abwere kwanuko pamodzi ndi abale. Sichinali cholinga chake kuti abwere panopa, koma adzabwera akadzapeza mpata.

13 Khalani maso,+ khalani ndi chikhulupiriro cholimba,+ khalani olimba mtima*+ ndipo khalani amphamvu.+ 14 Zonse zimene mukuchita, muzizichita mwachikondi.+

15 Abale, mukudziwa kuti anthu a mʼbanja la Sitefana ndi amene anali oyamba kukhala okhulupirira* ku Akaya ndipo anadzipereka kutumikira oyera. Choncho ndikukulimbikitsani kuti, 16 inunso pitirizani kukhala ogonjera kwa anthu ngati amenewo, ndi kwa aliyense amene akugwira nawo ntchitoyi mwakhama.+ 17 Koma ndikusangalala kuti Sitefana,+ Fotunato ndi Akayiko ndili nawo kuno, chifukwa alowa mʼmalo mwanu. 18 Anthu amenewa andilimbikitsa kwambiri ineyo komanso alimbikitsa inuyo. Choncho anthu otere muziwalemekeza.

19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni. Akula ndi Purisika komanso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa nonsenu, mwa Ambuye. 20 Abale onse akukupatsani moni. Mupatsane moni mwachikondi.

21 Tsopano landirani moni wanga, wa ineyo Paulo, wolemba ndekha ndi dzanja langa.

22 Aliyense amene sakonda Ambuye, atembereredwe. Bwerani Ambuye wathu! 23 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu kukhale nanu. 24 Ndikukutsimikizirani inu nonse amene ndinu ophunzira a Khristu Yesu kuti ndimakukondani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena