Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 4
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Masomphenya a Yehova ali kumwamba (1-11)

        • Yehova wakhala pampando wake wachifumu (2)

        • Akulu 24 akhala pamipando yachifumu (4)

        • Angelo 4 (6)

Chivumbulutso 4:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 74

Chivumbulutso 4:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 22:19; Yes 6:1; Eze 1:26, 27; Da 7:9; Mac 7:55

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 74-76

Chivumbulutso 4:3

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “mwala wofiira wamtengo wapatali.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 21:10, 11
  • +1Yo 1:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 6 2016, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 76

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2005, tsa. 31

Chivumbulutso 4:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:10; 5:8; 11:16; 19:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 76-77, 102-103, 288-289

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1995, tsa. 13

Chivumbulutso 4:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 1:13
  • +Eks 19:16
  • +Chv 1:4; 5:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 77-79

Chivumbulutso 4:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 30:18; 1Mf 7:23
  • +Eze 1:5-10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 79-80

Chivumbulutso 4:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 28:1; Yes 31:4
  • +Yob 39:9-11; Chv 6:3
  • +Chv 6:5
  • +Chv 6:7
  • +Yob 39:27, 29; Eze 1:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 80-81

Chivumbulutso 4:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 10:9, 12
  • +Yes 6:2, 3
  • +Chv 1:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 81, 129

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1986, tsa. 15

Chivumbulutso 4:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 90:2; Da 12:7

Chivumbulutso 4:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81

Chivumbulutso 4:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:16; Chv 14:7
  • +Chv 19:10
  • +Chv 5:13; 7:12; 11:17; 12:10
  • +Chv 10:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/2008, tsa. 31

    12/1/1999, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 4:21Mf 22:19; Yes 6:1; Eze 1:26, 27; Da 7:9; Mac 7:55
Chiv. 4:3Chv 21:10, 11
Chiv. 4:31Yo 1:5
Chiv. 4:4Chv 4:10; 5:8; 11:16; 19:4
Chiv. 4:5Eze 1:13
Chiv. 4:5Eks 19:16
Chiv. 4:5Chv 1:4; 5:6
Chiv. 4:6Eks 30:18; 1Mf 7:23
Chiv. 4:6Eze 1:5-10
Chiv. 4:7Miy 28:1; Yes 31:4
Chiv. 4:7Yob 39:9-11; Chv 6:3
Chiv. 4:7Chv 6:5
Chiv. 4:7Chv 6:7
Chiv. 4:7Yob 39:27, 29; Eze 1:10
Chiv. 4:8Eze 10:9, 12
Chiv. 4:8Yes 6:2, 3
Chiv. 4:8Chv 1:4
Chiv. 4:9Sl 90:2; Da 12:7
Chiv. 4:10Chv 5:8
Chiv. 4:11Mt 5:16; Chv 14:7
Chiv. 4:11Chv 19:10
Chiv. 4:11Chv 5:13; 7:12; 11:17; 12:10
Chiv. 4:11Chv 10:6
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 4:1-11

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

4 Zimenezi zitatha, ndinayangʼana kumwamba ndipo ndinaona khomo lotseguka. Mawu oyamba amene ndinamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga. Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno ndipo ndikuonetsa zinthu zimene zikuyenera kuchitika.” 2 Kenako nthawi yomweyo mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito mwa ine ndipo mpando wachifumu unaoneka uli pamalo ake kumwamba, wina atakhalapo.+ 3 Amene anakhala pampandoyo ankaoneka ngati mwala wa yasipi+ komanso mwala wa sadiyo.* Utawaleza wooneka ngati mwala wa emarodi unazungulira mpando wachifumuwo.+

4 Kuzungulira mpando wachifumuwo panalinso mipando yachifumu yokwana 24. Pamipando yachifumuyo, ndinaona patakhala akulu 24+ atavala zovala zoyera komanso zisoti zachifumu zagolide kumutu kwawo. 5 Kumpando wachifumuko kunkatuluka mphezi,+ mawu komanso mabingu.+ Panalinso nyale zamoto 7 zimene zinkayaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Nyalezo zikuimira mizimu 7 ya Mulungu.+ 6 Patsogolo pa mpando wachifumuwo, panali chinachake chooneka ngati nyanja ya galasi+ komanso ngati mwala wa kulusitalo.

Pakati pa mpando wachifumuwo ndiponso kuzungulira mpandowo, panali angelo 4+ amene anali ndi maso ambirimbiri, kutsogolo ndi kumbuyo komwe. 7 Mngelo woyamba ankaoneka ngati mkango.+ Mngelo wachiwiri ankaoneka ngati mwana wa ngʼombe wamphongo.+ Mngelo wachitatu+ anali ndi nkhope yooneka ngati ya munthu ndipo mngelo wa 4+ ankaoneka ngati chiwombankhanga chimene chikuuluka.+ 8 Aliyense wa angelo 4 amenewa anali ndi mapiko 6 ndipo mapikowo anali ndi maso paliponse.+ Angelo amenewa sankapuma masana ndi usiku, ankangokhalira kunena kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova*+ Mulungu, Wamphamvuyonse, amene analipo, amene alipo ndi amene akubwera.”+

9 Nthawi zonse angelowo akamapereka ulemerero ndi ulemu ndiponso akamayamikira Mulungu amene wakhala pampando wachifumuyo, Amene adzakhale ndi moyo kwamuyaya,+ 10 akulu 24 aja+ ankagwada nʼkuwerama pamaso pa Amene wakhala pampando wachifumuyo, nʼkulambira Amene adzakhale ndi moyo kwamuyayayo. Iwo ankaponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo nʼkunena kuti: 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu kulandira ulemerero,+ ulemu+ ndi mphamvu+ chifukwa munalenga zinthu zonse+ ndipo mwa kufuna kwanu, zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena