Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 4:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona.

  • 1 Samueli 20:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Mtumikiyo anapitadi. Zitatero, Davide anatulukira pafupi, chakum’mwera. Ndiyeno anagwada ndi kugunditsa nkhope yake pansi+ n’kuwerama katatu. Atatero, anayamba kupsompsonana+ ndi kulirirana mpaka Davide analira kwambiri kuposa Yonatani.+

  • Luka 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho ananyamukadi n’kupita kwa bambo ake. Ali chapatali ndithu, bambo akewo anamuona ndipo anagwidwa chifundo. Pamenepo anamuthamangira ndi kumukumbatira ndipo anamupsompsona mwachikondi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena