Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano Labani atangomva za Yakobo, mwana wa mlongo wake, anathamanga kukakumana naye.+ Atafika, anam’kumbatira ndi kum’psompsona, n’kupita naye kunyumba kwake.+ Kumeneko, Yakobo anafotokozera Labani zinthu zonse.

  • Genesis 45:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo Yosefe anayamba kupsompsona abale ake onsewo n’kumalira akuwakumbatira.+ Pambuyo pake, abale akewo analankhula naye.

  • 1 Samueli 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+

  • 2 Samueli 19:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Tsopano anthu onse anayamba kuwoloka Yorodano, ndipo mfumu nayonso inawoloka. Koma mfumu inapsompsona+ Barizilai ndi kumudalitsa,+ kenako Barizilai anabwerera kwawo.

  • Machitidwe 20:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pamenepo onse analira kwambiri, ndipo anakumbatira+ Paulo ndi kumupsompsona mwachikondi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena