Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine nditsikira kumeneko+ kudzalankhula nawe.+ Ndidzatengako gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe n’kuuika pa iwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyang’anira anthuwo, kuti usausenze wekhawekha.+

  • Deuteronomo 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+

  • Machitidwe 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero abale, fufuzani+ pakati panu amuna 7 a mbiri yabwino, amene ali ndi mzimu komanso nzeru zochuluka,+ kuti ife tiwaike kukhala oyang’anira ntchito yofunikayi.

  • 1 Timoteyo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+

  • Tito 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena