Deuteronomo 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Salimo 94:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amapha mkazi wamasiye ndi mlendo wokhala m’dziko lawo,+Ndipo amaphanso ana amasiye.*+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ Ezekieli 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anyoza abambo ndi amayi awo mwa iwe.+ Mlendo wokhala mwa iwe amuchitira zinthu mwachinyengo.+ Azunza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.”’”+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+
19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
7 Anthu anyoza abambo ndi amayi awo mwa iwe.+ Mlendo wokhala mwa iwe amuchitira zinthu mwachinyengo.+ Azunza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.”’”+
27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+