Ekisodo 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula. 1 Mbiri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+
21 Tsopano izi ndiye zinthu zonse zimene anawerengera za chihema chopatulika, chihema cha Umboni,+ monga mwa ntchito ya Alevi,+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. Iwo anawerengera zimenezi Mose atalamula.
3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+