Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero Aisiraeli anayamba kupembedza nawo Baala wa ku Peori.+ Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unawayakira.+

  • Nehemiya 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 chifukwa iwowa sanachingamire ana a Isiraeli kuti awapatse chakudya+ ndi madzi.+ M’malomwake, analemba ganyu Balamu+ kuti awatemberere.+ Koma Mulungu wathu anasintha temberero limenelo kukhala dalitso.+

  • 2 Petulo 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Popeza anasiya njira yowongoka, asocheretsedwa. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anakonda mphoto ya kuchita zoipa,+

  • Yuda 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena