Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kenako Leya anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamutcha Rubeni,*+ popeza anati: “N’chifukwa chakuti Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda kwambiri.”

  • Genesis 49:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Rubeni, iwe ndiwe mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka.+ Unayenera kukhala ndi ulemu wopambana ndi mphamvu zopambana.

  • Numeri 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mwera. Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.

  • 1 Mbiri 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mwana woyamba wa Isiraeli anali Rubeni.+ Iye anali woyamba kubadwa+ koma chifukwa chakuti anaipitsa bedi la bambo wake,+ udindo wake monga woyamba kubadwa unaperekedwa kwa ana a Yosefe,+ mwana wa Isiraeli. Choncho iye sanalembedwe monga woyamba kubadwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena