Ekisodo 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa m’dziko lokhalidwa ndi anthu.+ Mana ndiwo anali chakudya chawo mpaka pamene anafika m’malire a dziko la Kanani.+ Numeri 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho iwo anayamba kuwiringula kwa Mulungu+ ndiponso Mose,+ kuti: “Munatitulutsiranji m’dziko la Iguputo? Kodi mumafuna kuti tidzafere m’chipululu?+ Kuno chakudya kulibe, madzinso kulibe.+ Chakudya chonyansachi chafika potikola.”+
35 Ndipo ana a Isiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa m’dziko lokhalidwa ndi anthu.+ Mana ndiwo anali chakudya chawo mpaka pamene anafika m’malire a dziko la Kanani.+
5 Choncho iwo anayamba kuwiringula kwa Mulungu+ ndiponso Mose,+ kuti: “Munatitulutsiranji m’dziko la Iguputo? Kodi mumafuna kuti tidzafere m’chipululu?+ Kuno chakudya kulibe, madzinso kulibe.+ Chakudya chonyansachi chafika potikola.”+