Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho ndinatenga mdzakazi wanga ndi kum’duladula, n’kutumiza ziwalozo m’dera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinatero chifukwa iwo anachita khalidwe lotayirira+ komanso chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli.+

  • Oweruza 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo m’mafuko onse a Isiraeli titengemo amuna 10 mwa amuna 100 alionse, amuna 100 mwa amuna 1,000 alionse, amuna 1,000 mwa amuna 10,000 alionse. Amenewa azipezera anthu zofunika, kuti anthuwo achitepo kanthu mwa kupita ndi kukamenyana ndi Gibeya wa ku Benjamini, chifukwa cha chinthu chochititsa manyazi ndi chopusa+ chimene achita mu Isiraeli.”

  • 2 Samueli 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma Tamara anamuuza kuti: “Ayi, m’bale wanga! Usandichititse manyazi,+ chifukwa zimenezi n’zachilendo mu Isiraeli.+ Usachite chinthu chopusa, chochititsa manyazi ngati chimenechi.+

  • Aheberi 13:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena