Levitiko 11:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Deuteronomo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+ Mlaliki 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+ 1 Akorinto 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ndipo Mulungu amaweruza amene ali kunja?+ “M’chotseni pakati panu munthu woipayo.”+
45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+
7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+
13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+