Ekisodo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ngati sanachite kum’dikirira, ndipo Mulungu woona walola kuti mwangozi munthuyo afere m’manja mwake,+ pamenepo ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+ Numeri 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Mukapatse Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako.+ Kuwonjezera pa mizindayi, mukapatse Aleviwo mizinda ina 42. Numeri 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, m’dziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako. Deuteronomo 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pa nthawi imeneyo, Mose anapatula mizinda itatu kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano,+
13 Koma ngati sanachite kum’dikirira, ndipo Mulungu woona walola kuti mwangozi munthuyo afere m’manja mwake,+ pamenepo ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+
6 “Mukapatse Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako.+ Kuwonjezera pa mizindayi, mukapatse Aleviwo mizinda ina 42.
14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, m’dziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako.