Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+ 2 Mbiri 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo.+ Khalani m’malo anu, imani chilili+ ndi kuona Yehova akukupulumutsani.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+
13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+
17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo.+ Khalani m’malo anu, imani chilili+ ndi kuona Yehova akukupulumutsani.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+