2 Samueli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu inati: “Kodi palibe aliyense wotsala m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha kwa Mulungu.”+ Poyankha Ziba anauza mfumu kuti: “Alipo mwana wamwamuna wa Yonatani, wolumala mapazi.”+ 2 Samueli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+
3 Ndiyeno mfumu inati: “Kodi palibe aliyense wotsala m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha kwa Mulungu.”+ Poyankha Ziba anauza mfumu kuti: “Alipo mwana wamwamuna wa Yonatani, wolumala mapazi.”+
7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+