1 Samueli 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Motero anafunsiranso+ kwa Yehova, kuti: “Kodi mwamunayu wafika kale pano?” Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Uyu wabisala+ pakati pa katunduyu.” 1 Samueli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu+ wake m’manja mwa munthu wosamalira katundu,+ ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika kumeneko, anayamba kufunsa za abale ake ngati ali bwino.+ 1 Samueli 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndani angamve zimene mukunenazo? Pakuti gawo limene munthu amene anapita kunkhondo alandire, likhala lofanana ndi gawo limene munthu amene anali kulondera katundu alandire.+ Aliyense alandirapo kenakake.”+
22 Motero anafunsiranso+ kwa Yehova, kuti: “Kodi mwamunayu wafika kale pano?” Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Uyu wabisala+ pakati pa katunduyu.”
22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu+ wake m’manja mwa munthu wosamalira katundu,+ ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika kumeneko, anayamba kufunsa za abale ake ngati ali bwino.+
24 Ndani angamve zimene mukunenazo? Pakuti gawo limene munthu amene anapita kunkhondo alandire, likhala lofanana ndi gawo limene munthu amene anali kulondera katundu alandire.+ Aliyense alandirapo kenakake.”+