1 Mafumu 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo ananyamuka masana pamene Beni-hadadi anali kumwa ndi kuledzera+ m’misasa, pamodzi ndi mafumu ena 32 amene anali kumuthandiza aja. Miyambo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+ Hoseya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dama, vinyo wakale ndi vinyo wotsekemera zimawononga nzeru za munthu.+ 1 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akuba, aumbombo,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+ Aefeso 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiponso, musamaledzere naye vinyo,+ mmene muli makhalidwe oipa,+ koma khalanibe odzaza ndi mzimu.+
16 Iwo ananyamuka masana pamene Beni-hadadi anali kumwa ndi kuledzera+ m’misasa, pamodzi ndi mafumu ena 32 amene anali kumuthandiza aja.
20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+
18 Ndiponso, musamaledzere naye vinyo,+ mmene muli makhalidwe oipa,+ koma khalanibe odzaza ndi mzimu.+