1 Samueli 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+ 1 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+ Hoseya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinakupatsa mfumu nditakwiya+ ndipo ndidzaichotsa nditakwiya.+
10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+
13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+