27 Ndiyeno munthu wa Mulungu+ anapita kwa Eli ndi kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinadzisonyeze kunyumba ya kholo lako pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+
13Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+