Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide+ ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+

  • 1 Mafumu 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pa nthawi imeneyo Solomo+ anauza akulu,+ mitu yonse ya mafuko,+ ndi atsogoleri a makolo+ a ana a Isiraeli, kuti asonkhane+ kwa Mfumu Solomo ku Yerusalemu. Anawauza kuti akatenge likasa la pangano+ la Yehova ku Mzinda wa Davide,+ kutanthauza Ziyoni.+

  • 1 Mbiri 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano Davide anakambirana ndi mkulu aliyense wa anthu 1,000, wa anthu 100 ndiponso mtsogoleri aliyense.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena