2 Samueli 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wabwera dzulo lomweli, kodi lero uyende+ ndi ife kupita kulikonse kumene ine ndikupita? Bwerera, tenga abale ako ndi kubwerera nawo limodzi, ndipo Yehova akusonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi kukhulupirika kwake!”+ Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+ Salimo 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+
20 Iwe wabwera dzulo lomweli, kodi lero uyende+ ndi ife kupita kulikonse kumene ine ndikupita? Bwerera, tenga abale ako ndi kubwerera nawo limodzi, ndipo Yehova akusonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi kukhulupirika kwake!”+
11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+
3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+