Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadi

      Kwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+

  • Salimo 57:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+

      Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]

      Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+

  • Salimo 61:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mfumuyo idzakhala pamaso pa Mulungu mpaka kalekale.+

      Isonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha ndi kuipatsa choonadi kuti zimenezi ziiteteze.+

  • Salimo 85:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zakumana.+

      Chilungamo ndi mtendere zapsompsonana.+

  • Salimo 89:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+

      Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena