Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Achinyamata amene anakulira naye limodziwo anamuuza kuti: “Izi n’zimene mukanene kwa anthu awa amene akuuzani kuti, ‘Bambo anu anatisenzetsa goli lolemera, koma inuyo mutipeputsireko.’ Muwauze kuti,+ ‘Chala changa chaching’ono chidzakhala chachikulu kuposa chiuno cha bambo anga.+

  • Salimo 140:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wolankhula zazikulu* asakhazikike padziko lapansi.+

      Zoipa zisakesake munthu wochita zachiwawa ndipo zimukanthe mobwerezabwereza.+

  • Miyambo 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Milomo ya munthu wopusa imalowa mu mkangano,+ ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+

  • Miyambo 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kudzikuza kwa munthu wochokera kufumbi kudzamutsitsa,+ koma wa mtima wodzichepetsa adzapeza ulemerero.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena