Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.

  • 1 Mafumu 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pomalizira pake, Asa anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake.+ Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.

  • 1 Mafumu 22:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Pomalizira pake, Yehosafati anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide+ kholo lake. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena