-
2 Mbiri 12:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mfumu Rehobowamu inapitiriza kulimbitsa ufumu wake ndi kulamulira ku Yerusalemu. Rehobowamu+ anali ndi zaka 41 pamene anayamba kulamulira, ndipo kwa zaka 17 analamulira ku Yerusalemu, mzinda+ umene Yehova anasankha pakati pa mafuko onse a Isiraeli kuti aike dzina lake kumeneko.+ Mayi ake dzina lawo linali Naama+ Muamoni.+
-