1 Mafumu 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hiramu+ mfumu ya ku Turo+ inatumiza atumiki+ ake kwa Solomo, pakuti inamva kuti iyeyo ndi amene anadzozedwa kulowa ufumu m’malo mwa bambo ake, popeza Hiramuyo ankamukonda Davide masiku ake onse.+ 1 Mafumu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Hiramu+ atangomva mawu a Solomo, anasangalala kwambiri ndipo ananena kuti: “Yehova atamandike+ lero, popeza wapereka kwa Davide mwana wanzeru+ woti alamulire anthu ochulukawa.”+ 2 Mbiri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu+ mfumu ya Turo, kuti: “Monga momwe munachitira ndi Davide+ bambo anga pomawatumizira mitengo ya mkungudza kuti amangire nyumba yawo yokhalamo . . .
5 Hiramu+ mfumu ya ku Turo+ inatumiza atumiki+ ake kwa Solomo, pakuti inamva kuti iyeyo ndi amene anadzozedwa kulowa ufumu m’malo mwa bambo ake, popeza Hiramuyo ankamukonda Davide masiku ake onse.+
7 Hiramu+ atangomva mawu a Solomo, anasangalala kwambiri ndipo ananena kuti: “Yehova atamandike+ lero, popeza wapereka kwa Davide mwana wanzeru+ woti alamulire anthu ochulukawa.”+
3 Ndipo Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu+ mfumu ya Turo, kuti: “Monga momwe munachitira ndi Davide+ bambo anga pomawatumizira mitengo ya mkungudza kuti amangire nyumba yawo yokhalamo . . .