Genesis 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+ Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo. Salimo 60:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+
37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+
17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.
8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+