Salimo 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha, sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula, sindikutsegula pakamwa.+ Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+ Mlaliki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi yong’amba+ ndi nthawi yosoka.+ Nthawi yokhala chete+ ndi nthawi yolankhula.+
13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha, sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula, sindikutsegula pakamwa.+
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+