Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ukakana, nditumiza miliri yanga yonse pa iwe, pa atumiki ako ndi anthu ako, kuti udziwe kuti palibe wofanana ndi ine padziko lonse lapansi.+

  • Yoswa 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwo anamuyankha kuti: “Akapolo anufe tachokera kudziko lakutali kwambiri.+ Tabwera chifukwa tamva za dzina+ la Mulungu wanu, Yehova. Tamva mbiri yake ndi zonse zimene anachita ku Iguputo.+

  • 1 Samueli 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsoka ife! Adzatipulumutsa ndani m’manja mwa Mulungu wamkuluyu? Ameneyu ndi Mulungu amene anakantha Iguputo ndi masautso amtundu uliwonse m’chipululu.+

  • Yesaya 37:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kodi sunamve?+ Kuyambira nthawi zakale izi n’zimene ndidzachite.+

      Ndinakonza zimenezi kuyambira masiku amakedzana.+ Tsopano ndizichita.+

      Iweyo udzagwira ntchito yosandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, kukhala yopanda anthu ngati milu ya mabwinja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena