16 ku Hamati,+ ku Berota,+ ku Siburaimu kumene ndi kumalire a Damasiko+ ndi Hamati. Malirewo akafikenso ku Hazere-hatikoni kufupi ndi malire a Haurani.+
14 Tsopano Yehova, Mulungu wa makamu wanena kuti, ‘Inu a m’nyumba ya Isiraeli, ine ndikukudzutsirani mtundu wa anthu+ umene udzakuponderezani kuyambira kumalire ndi Hamati+ mpaka kuchigwa cha Araba.’”