2 Samueli 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+ 2 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+
23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+
10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+