Ekisodo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ 2 Mafumu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana+ ndi Yehova.” Chotero Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo atakwera m’galeta lankhondo la Yehu. 2 Mbiri 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anachotsa maguwa ansembe achilendo,+ anagwetsa malo okwezeka,+ anaphwanya zipilala zopatulika+ ndi kudula mizati yopatulika.+
24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+
16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana+ ndi Yehova.” Chotero Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo atakwera m’galeta lankhondo la Yehu.
3 Choncho iye anachotsa maguwa ansembe achilendo,+ anagwetsa malo okwezeka,+ anaphwanya zipilala zopatulika+ ndi kudula mizati yopatulika.+