Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo.

  • 2 Mbiri 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+

  • Miyambo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+

  • Danieli 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano Mulungu anawachititsa ana anayi amenewa kudziwa ndi kuzindikira zinthu zonse zolembedwa ndiponso anawapatsa nzeru.+ Danieli anali womvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena