Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.

  • Numeri 29:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 “‘Muzipereka zimenezi kwa Yehova pa zikondwerero zanu.+ Muzizipereka kuwonjezera pa zopereka zanu zalonjezo,+ ndi nsembe zanu zaufulu+ zimene mumapereka monga nsembe zanu zopsereza,+ nsembe zanu zambewu,+ nsembe zanu zachakumwa,+ ndi nsembe zanu zachiyanjano.’”+

  • Deuteronomo 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo.

  • 2 Mbiri 29:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pomalizira pake Hezekiya anati: “Tsopano mwayeneretsedwa kuti mukhale ansembe+ otumikira Yehova. Bweretsani nsembe zoyamikira+ ndi nsembe zina+ kunyumba ya Yehova.” Ndiyeno mpingowo unayamba kubweretsa nsembe zoyamikira ndi nsembe zina, ndipo aliyense wa mtima wofunitsitsa anali kubweretsa nsembe zopsereza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena