-
Yesaya 18:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Limeneli ndi dziko lomwe limatumiza nthumwi zake+ panyanja, m’ngalawa zoyenda pamadzi zopangidwa ndi gumbwa.* Limauza nthumwizo kuti: “Inu amithenga achangu, pitani ku mtundu wa anthu ataliatali osalala, anthu oopedwa ndi mitundu yonse ya anthu. Umenewu ndi mtundu wa anthu amphamvu kwambiri, ndiponso wopambana pa nkhondo, umene nthaka yake yakokoloka ndi mitsinje.”+
-