Yesaya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wamkazi wa Ziyoni+ wasiyidwa ngati msasa m’munda wa mpesa, ngati chisimba* m’munda wa minkhaka, ndiponso ngati mzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+ Maliro 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wapasula chisimba*+ chake ngati chisimba cha m’munda+ ndipo wathetsa zikondwerero zake.Yehova wachititsa kuti zikondwerero+ ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo mu mkwiyo wake waukulu wakana mfumu ndi wansembe.+
8 Mwana wamkazi wa Ziyoni+ wasiyidwa ngati msasa m’munda wa mpesa, ngati chisimba* m’munda wa minkhaka, ndiponso ngati mzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+
6 Iye wapasula chisimba*+ chake ngati chisimba cha m’munda+ ndipo wathetsa zikondwerero zake.Yehova wachititsa kuti zikondwerero+ ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo mu mkwiyo wake waukulu wakana mfumu ndi wansembe.+