Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+ Maliko 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno amene anali patsogolo ndi amene anali kubwera m’mbuyo anali kufuula kuti: “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!+ Chivumbulutso 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
9 Ndiyeno amene anali patsogolo ndi amene anali kubwera m’mbuyo anali kufuula kuti: “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!+
10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+