Salimo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khalani wofunitsitsa kundilanditsa, inu Yehova.+Inu Yehova, fulumirani kundithandiza.+ Salimo 70:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+ Salimo 71:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, musakhale kutali ndi ine.+Inu Mulungu wanga, fulumirani kundithandiza.+
5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+