Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+

      Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu.

  • Mlaliki 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 limene ndakhala ndikulifunafuna koma osalipeza. Pa anthu 1,000, ndapezapo mwamuna mmodzi yekha wowongoka mtima,+ koma pa anthu onsewa sindinapezepo mkazi wowongoka mtima.+

  • Yeremiya 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pitani mukayendeyende m’misewu ya mu Yerusalemu kuti mukaone, mukafufuze m’mabwalo ake ndi kudziwa ngati mungapezeke munthu,+ ngati muli aliyense wochita chilungamo,+ kapena aliyense wokhulupirika.+ Ngati mungamupeze munthu woteroyo, ndidzaukhululukira mzinda umenewu.

  • Mika 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+

  • Luka 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndithu ndikukuuzani, Iye adzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa iwo mwamsanga.+ Koma, Mwana wa munthu akadzafika, kodi adzapezadi chikhulupiriro padziko lapansi?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena