Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Potsirizira pake anati: “Chonde Yehova, pepani, musandipsere mtima,+ tandilolani ndilankhule komaliza kokhaka.+ Nanga mutapezeka 10?” Iye anayankha kuti: “Sindiwononga mzindawo chifukwa cha 10 amenewo.”+

  • Salimo 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+

      Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu.

  • Salimo 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Onse apatuka,+ ndipo onsewo ndi achinyengo.+

      Palibe aliyense amene akuchita zabwino,+

      Palibiretu ndi mmodzi yemwe.+

  • Ezekieli 22:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Anthu a m’dzikolo abera anthu pochita zachinyengo+ ndiponso zauchifwamba.+ Iwo akuzunza anthu osautsika ndi osauka.+ Abera mlendo pochita zachinyengo komanso zopanda chilungamo.’+

  • Amosi 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mukuweruza mopanda chilungamo,+ choncho moyo wakhala wowawa ndi wosautsa kwa anthu, pakuti inuyo mwakana chilungamo.+

  • Mika 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena