Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wafukula dzenje, walikumbadi.+Koma adzagwera m’dzenje lokumba yekha.+ Salimo 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Modzikweza, woipa amathamangitsa wosautsika,+Ndipo wosautsikayo amakodwa ndi maganizo amene woipa walingalira.+ Miyambo 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Woipa amangofunafuna kupanduka,+ ndipo munthu amene watumidwa kuti akamulange sam’chitira chifundo.+
2 Modzikweza, woipa amathamangitsa wosautsika,+Ndipo wosautsikayo amakodwa ndi maganizo amene woipa walingalira.+
11 Woipa amangofunafuna kupanduka,+ ndipo munthu amene watumidwa kuti akamulange sam’chitira chifundo.+