Salimo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti akuchitirani zinthu zoipa.+Alinganiza kuchita zinthu zimene sangazikwanitse.+ Miyambo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu angaganize za njira zake mumtima mwake,+ koma Yehova ndiye amawongolera mayendedwe ake.+ Miyambo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+ Miyambo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mayendedwe a mwamuna wamphamvu amachokera kwa Yehova,+ koma kodi munthu wochokera kufumbi angazindikire bwanji njira yake?+ 1 Akorinto 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma ngati wina ndi wokhazikika mumtima mwake ndipo alibe chomuvutitsa, koma amatha kulamulira mtima wake, ndipo wasankha mumtima mwake kukhalabe wosakwatira,* wachita bwino.+
21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+
24 Mayendedwe a mwamuna wamphamvu amachokera kwa Yehova,+ koma kodi munthu wochokera kufumbi angazindikire bwanji njira yake?+
37 Koma ngati wina ndi wokhazikika mumtima mwake ndipo alibe chomuvutitsa, koma amatha kulamulira mtima wake, ndipo wasankha mumtima mwake kukhalabe wosakwatira,* wachita bwino.+