Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno Mulungu anaona kuti zonse zimene anapanga zinali zabwino kwambiri.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku la 6.

  • Mlaliki 7:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Zimene ndapeza n’zakuti, Mulungu woona anapanga anthu owongoka mtima,+ koma anthuwo asankha njira zina zambirimbiri.”+

  • Maliko 7:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Inde, iwo anali kudabwa kwambiri+ ndipo anali kunena kuti: “Wachita zinthu zonse bwinobwino ndithu. Ngakhale ogontha akumva ndipo osalankhula akuwalankhulitsa.”+

  • Aroma 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chilengedwere dziko kupita m’tsogolo,+ makhalidwe a Mulungu osaoneka+ ndi maso akuonekera bwino. Makhalidwe a Mulungu amenewa, ngakhalenso mphamvu zake zosatha+ ndiponso Umulungu+ wake, zikuonekera m’zinthu zimene anapanga+ moti anthuwo alibenso chifukwa chomveka chosakhulupirira kuti kuli Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena