Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+

  • Hoseya 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Bzalani mbewu za chilungamo+ ndipo kololani zipatso za kukoma mtima kosatha.+ Limani munda panthaka yabwino+ pamene muli ndi nthawi yofunafuna Yehova, kufikira iye atabwera+ ndi kukupatsani malangizo onena za chilungamo.+

  • Yohane 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito.

  • 2 Akorinto 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ponena za nkhaniyi, wobzala moumira+ adzakololanso zochepa, ndipo wobzala mowolowa manja+ adzakololanso zochuluka.

  • Akolose 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena