Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 107:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Anthu owomboledwa a Yehova anene zimenezi,+

      Anthu amene iye wawawombola m’manja mwa mdani,+

  • Yesaya 62:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo adzatchedwa anthu oyera,+ owomboledwa ndi Yehova.+ Iweyo udzatchedwa “Mzinda Umene Anaufunafuna,” “Mzinda Umene Sanausiyiretu.”+

  • Agalatiya 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Khristu anatigula+ ndi kutimasula+ ku temberero la Chilamulo ndipo iyeyo anakhala temberero+ m’malo mwa ife, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wopachikidwa pamtengo.”+

  • Tito 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iyeyo anadzipereka+ m’malo mwa ife kuti atilanditse+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse,+ kuti tikhale anthu akeake,+ odzipereka pa ntchito zabwino.+

  • 1 Petulo 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pajatu mukudziwa kuti sizinali zinthu zotha kuvunda,+ siliva kapena golide, zimene zinakumasulani+ ku khalidwe lanu lopanda phindu limene munalilandira kuchokera kwa makolo anu mwa chikhalidwe chanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena