2 Mafumu 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwina Yehova Mulungu amva+ mawu onse a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yam’tuma, kuti adzatonze+ nawo Mulungu wamoyo. Ndipo mwina amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva.+ Inuyo mupereke pemphero+ m’malo mwa otsalira+ amene alipo.’” 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+ 2 Mbiri 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 lye analembanso makalata+ onyoza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ komanso omutonza kuti: “Mofanana ndi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena imene sinapulumutse anthu ake m’manja mwanga,+ Mulungu wa Hezekiya sapulumutsa anthu ake m’manja mwanga.”
4 Mwina Yehova Mulungu amva+ mawu onse a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yam’tuma, kuti adzatonze+ nawo Mulungu wamoyo. Ndipo mwina amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva.+ Inuyo mupereke pemphero+ m’malo mwa otsalira+ amene alipo.’”
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
17 lye analembanso makalata+ onyoza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ komanso omutonza kuti: “Mofanana ndi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena imene sinapulumutse anthu ake m’manja mwanga,+ Mulungu wa Hezekiya sapulumutsa anthu ake m’manja mwanga.”