Yesaya 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+ Ezekieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo avala ziguduli,*+ ndipo thupi lawo lonse likunjenjemera.+ Pankhope zawo zonse pali manyazi+ ndipo m’mitu yawo yonse muli mipala.+ Mika 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Meta mpala ndi kuchotsa tsitsi lonse chifukwa cha ana ako aamuna amene unali kuwakonda.+ Meta mpala mpaka ufanane ndi wa chiwombankhanga, chifukwa chakuti ana akowo akusiya ndipo apita kudziko lina.”+
12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+
18 Iwo avala ziguduli,*+ ndipo thupi lawo lonse likunjenjemera.+ Pankhope zawo zonse pali manyazi+ ndipo m’mitu yawo yonse muli mipala.+
16 Meta mpala ndi kuchotsa tsitsi lonse chifukwa cha ana ako aamuna amene unali kuwakonda.+ Meta mpala mpaka ufanane ndi wa chiwombankhanga, chifukwa chakuti ana akowo akusiya ndipo apita kudziko lina.”+